9 Choncho mwa njira imeneyi zolakwa za Yakobo zidzaphimbidwa,+
Ndipo tchimo lake likadzachotsedwa zotsatira zake zidzakhala izi:
Adzasandutsa miyala yonse yapaguwa lansembe
Kukhala ngati miyala yofewa kwambiri imene yanyenyekanyenyeka,
Ndipo sipadzatsala mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+