Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno anafuula mawu ochokera kwa Yehova otemberera guwalo, kuti: “Guwa lansembe iwe! Guwa lansembe iwe! Yehova wanena kuti, ‘Mwana wamwamuna adzabadwa mʼnyumba ya Davide, dzina lake Yosiya.+ Iye adzatenga ansembe a malo okwezeka amene akupereka nsembe yautsi pa iwe nʼkuwapereka nsembe pa iwe. Ndipo adzawotcha mafupa a anthu pa iwe.’”+

  • 2 Mafumu 23:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako inaitanitsa ansembe onse kuchokera mʼmizinda ya Yuda. Ndipo malo okwezeka amene ansembewo ankaperekako nsembe yautsi, kuyambira ku Geba+ mpaka ku Beere-seba,+ inawachititsa kuti akhale osayenera kulambirako. Inagwetsanso malo okwezeka a pageti amene anali pakhomo lapageti la Yoswa mkulu wa mzindawo. Getilo linali mbali ya kumanzere munthu akamalowa pageti la mzindawo.

  • 2 Mafumu 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Iye anapha ansembe onse a mʼmalo okwezeka nʼkuwapereka nsembe pamaguwa ansembe kumeneko. Kenako anawotcha mafupa a anthu pamaguwa ansembewo.+ Atatero anabwerera ku Yerusalemu.

  • Ezekieli 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mitembo ya Aisiraeli ndidzaiponyera pamaso pa mafano awo onyansa, ndipo mafupa anu ndidzawamwaza kuzungulira maguwa anu ansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena