Yoswa 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Aisiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo. Iwo azingogonja nʼkumathawa adani awo, chifukwa nawonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindikhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+ Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka mʼmanja mwa adani amene anawaukira nʼkutenga zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kulimbana nawo.+ Yeremiya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale mutapha pafupifupi asilikali onse a Akasidi amene akumenyana nanu nʼkungotsala ovulala kwambiri okha, iwo angadzukebe mʼmatenti awo nʼkuwotcha mzindawu ndi moto.”’”+
12 Choncho Aisiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo. Iwo azingogonja nʼkumathawa adani awo, chifukwa nawonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindikhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+
14 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka mʼmanja mwa adani amene anawaukira nʼkutenga zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kulimbana nawo.+
10 Ngakhale mutapha pafupifupi asilikali onse a Akasidi amene akumenyana nanu nʼkungotsala ovulala kwambiri okha, iwo angadzukebe mʼmatenti awo nʼkuwotcha mzindawu ndi moto.”’”+