-
Levitiko 13:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Wansembeyo aziona nthenda imene yatuluka pakhunguyo. Ngati cheya chapamalopo chasanduka choyera ndipo pakuoneka kuti nthendayo yalowa mpaka mkati mwa khungu, ndiye kuti limenelo ndi khate. Wansembe aziona nthendayo nʼkugamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa.
-
-
Levitiko 15:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Iye ndi wodetsedwa chifukwa cha zimene zikukhazo, kaya zinthuzo zikupitirizabe kutuluka kapena maliseche ake atsekeka ndi zimene zikukhazo, azikhalabe wodetsedwa.
-