Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+ Ekisodo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Mose anatenga magaziwo nʼkuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapangana nanu mogwirizana ndi mawu onsewa.”+ Deuteronomo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditakwera mʼphiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita ndi inu,+ ndinakhala mʼphirimo masiku 40, masana ndi usiku,+ ndipo sindinadye chakudya kapena kumwa madzi.
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
8 Choncho Mose anatenga magaziwo nʼkuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapangana nanu mogwirizana ndi mawu onsewa.”+
9 Nditakwera mʼphiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita ndi inu,+ ndinakhala mʼphirimo masiku 40, masana ndi usiku,+ ndipo sindinadye chakudya kapena kumwa madzi.