Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma ngati akupereka nyama yodetsedwa+ imene sikuyenera kuperekedwa nsembe kwa Yehova, azikaonetsa nyamayo kwa wansembe. 12 Wansembe azinena mtengo wake mogwirizana ndi mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo umene wansembe wanena uzikhala womwewo.

  • Levitiko 27:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma ngati akupereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika mʼChaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake womwe unaikidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena