-
Levitiko 27:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma ngati walonjeza kupereka nyama yomwe ndi yoyenera kuperekedwa nsembe kwa Yehova, nyama iliyonse imene angapereke kwa Yehova izikhala yopatulika. 10 Asaichotse nʼkuikapo ina, ndipo asasinthanitse yabwino ndi yoipa kapena yoipa ndi yabwino. Koma ngati waisinthanitsa ndi nyama ina, zonse ziwiri, yoyambayo ndiponso imene waisinthanitsayo, zizikhala zopatulika.
-