Levitiko 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafuta onse a mbuziyo aziwawotcha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yamgwirizano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo, ndipo adzakhululukidwa.
26 Mafuta onse a mbuziyo aziwawotcha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yamgwirizano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo, ndipo adzakhululukidwa.