Levitiko 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo zimene zatsala pansembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake, chifukwa ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova. Levitiko 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Lamulo la nsembe yakupalamula+ ndi ili: Nsembeyi ndi yopatulika koposa. Levitiko 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo+ ndipo aziidyera mʼmalo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+
10 Ndipo zimene zatsala pansembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake, chifukwa ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova.
6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo+ ndipo aziidyera mʼmalo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+