-
Levitiko 10:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Nʼchifukwa chiyani simunadye nsembe yamachimo mʼmalo oyera?+ Nsembe imeneyi ndi yopatulika koposa, ndipo Mulungu wakupatsani kuti munyamule zolakwa za gulu lonse, ndi kuphimba machimo a gulu lonseli pamaso pa Yehova. 18 Taonani, simunabweretse magazi ake mkati, mʼmalo oyera.+ Munafunika kudya nsembeyo mʼmalo oyera, mogwirizana ndi zimene Mulungu anandilamula.”
-