Ekisodo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mʼmwezi wachitatu kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo, tsiku lomwelo* iwo analowa mʼchipululu cha Sinai. Machitidwe 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ameneyu ndi amene anali ndi Aisiraeli mʼchipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu+ komanso makolo athu paphiri la Sinai. Iye analandira mawu opatulika omwe ndi amphamvu kuti atipatsire.+
19 Mʼmwezi wachitatu kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo, tsiku lomwelo* iwo analowa mʼchipululu cha Sinai.
38 Ameneyu ndi amene anali ndi Aisiraeli mʼchipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu+ komanso makolo athu paphiri la Sinai. Iye analandira mawu opatulika omwe ndi amphamvu kuti atipatsire.+