Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ omwe ndi ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira, nʼkuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Atatero anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule. 2 Choncho moto unatsika kuchokera kwa Yehova nʼkuwawotcha,+ moti anafa pamaso pa Yehova.+

  • Numeri 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mayina a ana a Aroni anali awa: woyamba Nadabu kenako Abihu,+ Eleazara+ ndi Itamara.+

  • Numeri 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova atapereka moto wosaloledwa kwa Yehova+ mʼchipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Pomwe Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo.

  • 1 Mbiri 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Nadabu ndi Abihu anamwalira opanda ana aamuna bambo awo adakali ndi moyo,+ koma Eliezara+ ndi Itamara ankatumikirabe ngati ansembe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena