Numeri 33:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kenako ananyamuka ku Alimoni-dibilataimu, nʼkukamanga msasa kumapiri a Abarimu,+ pafupi ndi Nebo.+ Deuteronomo 32:48, 49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova analankhula ndi Mose pa tsiku lomweli kuti: 49 “Kwera mʼphiri ili la Abarimu,+ phiri la Nebo,+ limene lili mʼdziko la Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko, ndipo uone dziko la Kanani limene ndikupereka kwa Aisiraeli kuti likhale lawo.+
47 Kenako ananyamuka ku Alimoni-dibilataimu, nʼkukamanga msasa kumapiri a Abarimu,+ pafupi ndi Nebo.+
48 Yehova analankhula ndi Mose pa tsiku lomweli kuti: 49 “Kwera mʼphiri ili la Abarimu,+ phiri la Nebo,+ limene lili mʼdziko la Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko, ndipo uone dziko la Kanani limene ndikupereka kwa Aisiraeli kuti likhale lawo.+