Genesis 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anapitiriza kuwadalitsa pa tsikulo+ kuti: “Aisiraeli akamadalitsana azidzatchula dzina lako kuti,‘Mulungu akudalitse ngati mmene anadalitsira Efuraimu ndi Manase.’” Choncho Isiraeli anapitiriza kuika Efuraimu patsogolo pa Manase.
20 Iye anapitiriza kuwadalitsa pa tsikulo+ kuti: “Aisiraeli akamadalitsana azidzatchula dzina lako kuti,‘Mulungu akudalitse ngati mmene anadalitsira Efuraimu ndi Manase.’” Choncho Isiraeli anapitiriza kuika Efuraimu patsogolo pa Manase.