Numeri 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kuchigwa cha Esikolo,*+ anadula nthambi yokhala ndi phava limodzi lalikulu la mphesa, ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi ndodo yonyamulira. Anatengakonso makangaza* ndi nkhuyu.+ Deuteronomo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho iwo ananyamuka nʼkupita kudera lamapiri+ mpaka anakafika kuchigwa cha Esikolo,* ndipo anazonda dzikolo.
23 Atafika kuchigwa cha Esikolo,*+ anadula nthambi yokhala ndi phava limodzi lalikulu la mphesa, ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi ndodo yonyamulira. Anatengakonso makangaza* ndi nkhuyu.+
24 Choncho iwo ananyamuka nʼkupita kudera lamapiri+ mpaka anakafika kuchigwa cha Esikolo,* ndipo anazonda dzikolo.