Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma chifukwa choti mtumiki wanga Kalebe+ anali wosiyana ndi ena,* ndipo wakhala akunditsatira ndi mtima wonse, ndithu ndidzamulowetsa mʼdziko limene anakalizonda, ndipo mbadwa zake zidzatenga dzikolo kukhala lawo.+

  • Deuteronomo 1:34-38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Nthawi yonseyi Yehova ankamva zimene munkanena ndipo anakwiya kwambiri, moti analumbira kuti,+ 35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a mʼbadwo woipa uwu amene adzaone dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+ 36 kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune. Iyeyu adzaliona, ndipo ndidzapereka dziko limene anafikako kwa iye ndi ana ake, chifukwa chakuti watsatira Yehova ndi mtima wonse.+ 37 (Ngakhale inenso Yehova anandikwiyira chifukwa cha inu, ndipo anati, “Iwenso sukalowa mʼdziko limeneli.+ 38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira+ ndi amene akalowe mʼdzikomo.+ Umulimbitse,*+ chifukwa ndi amene adzatsogolere Aisiraeli pokatenga dzikolo kukhala lawo.”)

  • Yoswa 14:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ngakhale kuti abale anga amene ndinali nawo, anapangitsa anthu kuchita mantha kwambiri,* ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena