Deuteronomo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa nthawi imeneyo ndinakulamulani kuti: ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna onse olimba mtima atenge zida ndipo awoloke patsogolo pa abale anu, Aisiraeli.+ Yoswa 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu a fuko la Rubeni, a fuko la Gadi komanso hafu ya fuko la Manase, anawoloka nʼkumayenda patsogolo pa Aisiraeli ena atakonzekera kumenya nkhondo,+ ngati mmene Mose anawalangizira.+
18 Pa nthawi imeneyo ndinakulamulani kuti: ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna onse olimba mtima atenge zida ndipo awoloke patsogolo pa abale anu, Aisiraeli.+
12 Anthu a fuko la Rubeni, a fuko la Gadi komanso hafu ya fuko la Manase, anawoloka nʼkumayenda patsogolo pa Aisiraeli ena atakonzekera kumenya nkhondo,+ ngati mmene Mose anawalangizira.+