Numeri 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako pazibwera fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidiyoni.
22 Kenako pazibwera fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidiyoni.