Ekisodo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atachoka ku Elimu, gulu lonse la Aisiraeli linafika mʼchipululu cha Sini chimene chili pakati pa Elimu ndi Sinai.+ Anafika kumeneko pa tsiku la 15 la mwezi wachiwiri atachoka mʼdziko la Iguputo.
16 Atachoka ku Elimu, gulu lonse la Aisiraeli linafika mʼchipululu cha Sini chimene chili pakati pa Elimu ndi Sinai.+ Anafika kumeneko pa tsiku la 15 la mwezi wachiwiri atachoka mʼdziko la Iguputo.