Ekisodo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Musadzaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo musadzatengere zochita zawo.+ Mʼmalomwake, mudzawononge mafano awo komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Ekisodo 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati* yawo yopatulika mukaidule.+ Ekisodo 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musapange milungu ya chitsulo chosungunula.+ Deuteronomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule mizati yawo yopatulika+ ndi kuwotcha zifaniziro zawo zogoba.+ Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+
24 Musadzaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo musadzatengere zochita zawo.+ Mʼmalomwake, mudzawononge mafano awo komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+
13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati* yawo yopatulika mukaidule.+
5 Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule mizati yawo yopatulika+ ndi kuwotcha zifaniziro zawo zogoba.+
3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+