Genesis 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwonjezera pamenepo, aliyense amene adzakupheni* ndidzamupatsa chilango. Ngati chamoyo chilichonse chapha munthu, chamoyocho chidzaphedwanso. Ndipo munthu aliyense wochotsa moyo wa mʼbale wake, ndidzamupatsa chilango.+ Ekisodo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu akamupsera mtima mnzake mpaka kumupha mwadala,+ munthuyo aziphedwa. Ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe, muzimuchotsa nʼkukamupha.+ Deuteronomo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musamamumvere* chisoni ndipo muzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendereni bwino.
5 Kuwonjezera pamenepo, aliyense amene adzakupheni* ndidzamupatsa chilango. Ngati chamoyo chilichonse chapha munthu, chamoyocho chidzaphedwanso. Ndipo munthu aliyense wochotsa moyo wa mʼbale wake, ndidzamupatsa chilango.+
14 Munthu akamupsera mtima mnzake mpaka kumupha mwadala,+ munthuyo aziphedwa. Ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe, muzimuchotsa nʼkukamupha.+
13 Musamamumvere* chisoni ndipo muzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendereni bwino.