Numeri 8:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma akakwanitsa zaka 50, azituluka mʼgululo ndipo asamatumikirenso. 26 Iye azingothandizira abale ake amene akugwira ntchito pachihema chokumanako, koma asamatumikire kuchihemako. Izi ndi zimene uzichita ndi Alevi mogwirizana ndi ntchito zawo.”+
25 Koma akakwanitsa zaka 50, azituluka mʼgululo ndipo asamatumikirenso. 26 Iye azingothandizira abale ake amene akugwira ntchito pachihema chokumanako, koma asamatumikire kuchihemako. Izi ndi zimene uzichita ndi Alevi mogwirizana ndi ntchito zawo.”+