Numeri 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako pazibwera fuko la Nafitali. Mtsogoleri wa ana a Nafitali ndi Ahira,+ mwana wa Enani. Numeri 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Nafitali anali Ahira,+ mwana wa Enani.