Ekisodo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Upange zitsulo 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu+ 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu lililonse kuti mulowe zolumikizira ziwiri.+ Ekisodo 38:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Popanga zitsulo za malo oyera zokhazikapo mafelemu ndi zitsulo zokhazikapo zipilala za makatani anagwiritsa ntchito matalente 100. Popanga zitsulo 100 anagwiritsa ntchito matalente 100, talente imodzi anapangira chitsulo chimodzi.+
19 Upange zitsulo 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu+ 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu lililonse kuti mulowe zolumikizira ziwiri.+
27 Popanga zitsulo za malo oyera zokhazikapo mafelemu ndi zitsulo zokhazikapo zipilala za makatani anagwiritsa ntchito matalente 100. Popanga zitsulo 100 anagwiritsa ntchito matalente 100, talente imodzi anapangira chitsulo chimodzi.+