-
Ekisodo 27:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Upangenso zipilala zake 20 ndi zitsulo 20 zakopa zokhazikapo zipilalazo. Tizitsulo ta zipilala tokolowekapo nsalu ndi tolumikizira take tikhale tasiliva.
-