Ekisodo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mʼmwezi woyamba wa chaka chachiwiri, pa tsiku loyamba la mweziwo, anamanga chihema.+