Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mundipangire malo opatulika, ndipo ndidzakhala pakati panu.+ Levitiko 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndidzaika chihema changa pakati panu,+ ndipo sindidzakukanani.