Levitiko 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usagone ndi mkazi wa mnzako nʼkukhala wodetsedwa.+ Deuteronomo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musachite chigololo.+