Genesis 30:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zilipa kapolo wa Leya, anaberekera Yakobo mwana wamwamuna. 11 Zitatero Leya anati: “Ndachita mwayi!” Choncho anapatsa mwanayo dzina lakuti Gadi.*+ Genesis 46:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana a Gadi+ anali Zifioni, Hagi, Suni, Eziboni, Eri, Arodi ndi Areli.+ Numeri 2:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako pazibwera fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli. 15 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 45,650.+
10 Zilipa kapolo wa Leya, anaberekera Yakobo mwana wamwamuna. 11 Zitatero Leya anati: “Ndachita mwayi!” Choncho anapatsa mwanayo dzina lakuti Gadi.*+
14 Kenako pazibwera fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli. 15 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 45,650.+