Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndamuberekera ana aamuna 6.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+ Numeri 2:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako pazibwera fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa ana a Zebuloni ndi Eliyabu,+ mwana wa Heloni. 8 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 57,400.+
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndamuberekera ana aamuna 6.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+
7 Kenako pazibwera fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa ana a Zebuloni ndi Eliyabu,+ mwana wa Heloni. 8 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 57,400.+