Numeri 2:20, 21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri. 21 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 32,200.+
20 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri. 21 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 32,200.+