-
Genesis 30:4-6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho Rakele anapereka kapolo wake Biliha kwa Yakobo kuti akhale mkazi wake, ndipo iye anagona naye.+ 5 Biliha anakhala woyembekezera ndipo patapita nthawi anamuberekera Yakobo mwana wamwamuna. 6 Ndiyeno Rakele anati: “Mulungu wakhala woweruza wanga komanso wamva mawu anga, ndipo wandipatsa mwana wamwamuna.” Nʼchifukwa chake Rakele anapatsa mwanayo dzina lakuti Dani.*+
-