Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ana amene Zilipa kapolo wa Leya anaberekera Yakobo anali Gadi ndi Aseri. Ana aamuna amene Yakobo anabereka ku Padani-aramu ndi amenewa.

  • Numeri 2:27, 28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani. 28 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 41,500.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena