29 Kenako pazibwera fuko la Nafitali. Mtsogoleri wa ana a Nafitali ndi Ahira,+ mwana wa Enani. 30 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 53,400.+
48 Ana aamuna a Nafitali+ potengera mabanja awo anali awa: Yahazeeli amene anali kholo la banja la Ayahazeeli, Guni amene anali kholo la banja la Aguni,