Numeri 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chihema chitapasulidwa,+ ana a Gerisoni+ ndi ana a Merari,+ amene ankanyamula chihemacho, ananyamuka. Numeri 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Akohati, amene ankanyamula zinthu za mʼmalo opatulika+ ananyamuka, kuti akamakafika akapeze chihema chitamangidwa kale.
17 Chihema chitapasulidwa,+ ana a Gerisoni+ ndi ana a Merari,+ amene ankanyamula chihemacho, ananyamuka.
21 Kenako Akohati, amene ankanyamula zinthu za mʼmalo opatulika+ ananyamuka, kuti akamakafika akapeze chihema chitamangidwa kale.