Numeri 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amene anapereka zopereka zake pa tsiku loyamba anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu, wa fuko la Yuda. Numeri 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, gulu la mafuko atatu la ana a Yuda ndi limene linali loyamba kunyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. Rute 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aminadabu+ anabereka Naasoni, Naasoni anabereka Salimoni, Mateyu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ramu anabereka Aminadabu.Aminadabu anabereka Naasoni.+Naasoni anabereka Salimoni.
12 Amene anapereka zopereka zake pa tsiku loyamba anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu, wa fuko la Yuda.
14 Choncho, gulu la mafuko atatu la ana a Yuda ndi limene linali loyamba kunyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.