-
2 Samueli 10:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Patapita nthawi, Aamoni anaona kuti akhala ngati chinthu chonunkha kwa Davide. Choncho anatumiza anthu kuti akalembe ganyu Asiriya a ku Beti-rehobu+ ndi Asiriya a ku Zoba+ ndipo onse pamodzi analipo asilikali 20,000 oyenda pansi. Anapitanso kwa mfumu ya ku Maaka+ nʼkulemba ganyu amuna 1,000 komanso ku Isitobu amuna 12,000.+
-
-
2 Samueli 10:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Aamoni anapita kukaima pageti la mzinda atakonzekera kumenya nkhondo. Pomwe Asiriya a ku Zoba, a ku Rehobu, a ku Isitobu ndi a ku Maaka anakayalana kwaokha kutchire.
-