Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano anthuwo anayamba kudandaula kwambiri pamaso pa Yehova. Yehova atamva kudandaulako mkwiyo wake unayaka, ndipo moto wochokera kwa Yehova unawayakira nʼkupsereza ena mwa anthuwo kumalire a msasa.

  • Numeri 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Kodi gulu la anthu oipa amenewa lingʼungʼudza motsutsana nane mpaka liti?+ Ndamva kungʼungʼudza kumene Aisiraeli akuchita motsutsana nane.+

  • Numeri 16:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha zimene mukuchitazi, iweyo limodzi ndi anthu onse amene akukutsatira, mukuukira Yehova. Kunena za Aroni, kodi iyeyo ndi ndani kuti mumudandaule?”+

  • 1 Akorinto 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+

  • 1 Akorinto 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tisakhalenso ongʼungʼudza, ngati mmene ena a iwo anachitira,+ nʼkuphedwa ndi mngelo wowononga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena