Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Upereke Alevi kwa Aroni ndi ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera kwa Aisiraeli.+

  • Numeri 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ine ndasankha Alevi pakati pa Aisiraeli mʼmalo mwa ana onse oyamba kubadwa* a Aisiraeli+ ndipo Aleviwo adzakhala anga.

  • Numeri 8:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pambuyo pake, Aleviwo azitumikira pachihema chokumanako. Uzichita zimenezi powayeretsa ndi kuwapereka monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku. 16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa Aisiraeli. Ine ndikuwatenga kukhala anga mʼmalo mwa onse oyamba kubadwa* pakati pa Aisiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena