Ekisodo 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana woyamba kubadwa wa bulu muzimuwombola ndi nkhosa. Koma ngati simungamuwombole, muzimuthyola khosi. Ndipo muziwombola mwana wanu wamwamuna aliyense woyamba kubadwa.+ Palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja. Levitiko 27:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma ngati ndi nyama yodetsedwa ndipo waiwombola mogwirizana ndi mtengo womwe unaikidwa, azipereka mtengo wa nyamayo nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+ Koma ngati sangaiwombole izigulitsidwa pa mtengo womwe unaikidwa.
20 Mwana woyamba kubadwa wa bulu muzimuwombola ndi nkhosa. Koma ngati simungamuwombole, muzimuthyola khosi. Ndipo muziwombola mwana wanu wamwamuna aliyense woyamba kubadwa.+ Palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.
27 Koma ngati ndi nyama yodetsedwa ndipo waiwombola mogwirizana ndi mtengo womwe unaikidwa, azipereka mtengo wa nyamayo nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+ Koma ngati sangaiwombole izigulitsidwa pa mtengo womwe unaikidwa.