2 Mbiri 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuwonjezera pamenepo, Hezekiya anauza anthu a ku Yerusalemu kuti azipereka gawo loyenera kupita kwa ansembe ndi Alevi+ nʼcholinga choti iwo azitsatira mosamala lamulo la Yehova.
4 Kuwonjezera pamenepo, Hezekiya anauza anthu a ku Yerusalemu kuti azipereka gawo loyenera kupita kwa ansembe ndi Alevi+ nʼcholinga choti iwo azitsatira mosamala lamulo la Yehova.