Ekisodo 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose+ kuti: “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukukangana ndi ine? Nʼchifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+
2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose+ kuti: “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukukangana ndi ine? Nʼchifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+