Ekisodo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi gulu lonse la Aisiraeli, iwo anatembenuka nʼkuyangʼana kuchipululu. Ndipo kenako ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+ Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma gulu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa Aisiraeli onse+ pamwamba pa chihema chokumanako.
10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi gulu lonse la Aisiraeli, iwo anatembenuka nʼkuyangʼana kuchipululu. Ndipo kenako ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+
10 Koma gulu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa Aisiraeli onse+ pamwamba pa chihema chokumanako.