Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Aliyense wa iwo anaponya pansi ndodo yake, ndipo zinasanduka njoka zazikulu. Koma ndodo ya Aroni inameza ndodo zawo.

  • Ekisodo 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tenga ndodo yako, utambasule dzanja lako nʼkuloza madzi a mu Iguputo.+ Uloze mitsinje yawo, ngalande zawo,* zithaphwi zawo+ ndi malo onse amene amasungira madzi kuti asanduke magazi.’ Choncho madzi amʼdziko lonse la Iguputo, ngakhalenso madzi amʼmitsuko yawo yamtengo ndi yamwala adzakhala magazi.”

  • Numeri 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Bwezera ndodo ya Aroni+ patsogolo pa Umboni. Uisunge kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana opandukawa,+ nʼcholinga chakuti asiye kungʼungʼudza motsutsana ndi ine komanso kuti asafe.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena