Salimo 106:32, 33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iwo anamukwiyitsanso pa madzi a ku Meriba,*Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+ 33 Iwo anamukwiyitsaNdipo Mose analankhula mosaganiza bwino.+
32 Iwo anamukwiyitsanso pa madzi a ku Meriba,*Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+ 33 Iwo anamukwiyitsaNdipo Mose analankhula mosaganiza bwino.+