Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Dzina lina la Esau linali Edomu.+ Deuteronomo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Auze anthuwo kuti: “Mudutsa mʼmalire a dziko la abale anu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri. Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musamadane ndi mbadwa ya Edomu, chifukwa ndi mʼbale wanu.+ Musamadane ndi munthu wa ku Iguputo, chifukwa munali alendo mʼdziko lawo.+
4 Auze anthuwo kuti: “Mudutsa mʼmalire a dziko la abale anu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri.
7 Musamadane ndi mbadwa ya Edomu, chifukwa ndi mʼbale wanu.+ Musamadane ndi munthu wa ku Iguputo, chifukwa munali alendo mʼdziko lawo.+