Ekisodo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anaika akapitawo oti aziwayangʼanira pa ntchito yawo yaukapolo kuti aziwazunza powagwiritsa ntchito mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.* Ekisodo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa, yomwe inali yoponda matope ndi kuumba njerwa. Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse mʼmunda. Ankawazunza komanso kuwagwiritsa ntchito ya mtundu uliwonse wa ukapolo.+
11 Choncho anaika akapitawo oti aziwayangʼanira pa ntchito yawo yaukapolo kuti aziwazunza powagwiritsa ntchito mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*
14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa, yomwe inali yoponda matope ndi kuumba njerwa. Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse mʼmunda. Ankawazunza komanso kuwagwiritsa ntchito ya mtundu uliwonse wa ukapolo.+