Ekisodo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aroni mʼbale wako umupangire zovala zopatulika kuti zimupatse ulemerero ndi kumʼkongoletsa.+ Ekisodo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zovala zopatulika+ za Aroni zidzagwiritsidwa ntchito ndi ana ake+ obwera mʼmbuyo mwake akadzawadzoza nʼkuwaika kuti akhale ansembe.
29 Zovala zopatulika+ za Aroni zidzagwiritsidwa ntchito ndi ana ake+ obwera mʼmbuyo mwake akadzawadzoza nʼkuwaika kuti akhale ansembe.