Numeri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkutibweretsa kumalo oipa ano?+ Kuno sikungamere mbewu iliyonse ndipo kulibe mitengo ya nkuyu, mitengo ya mpesa kapena mitengo ya makangaza. Ndi madzi akumwa omwe kulibe.”+
5 Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkutibweretsa kumalo oipa ano?+ Kuno sikungamere mbewu iliyonse ndipo kulibe mitengo ya nkuyu, mitengo ya mpesa kapena mitengo ya makangaza. Ndi madzi akumwa omwe kulibe.”+