Salimo 78:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo ankamufunafuna.+Iwo ankabwerera nʼkuyamba kufunafuna Mulungu,